Level 20 Level 22
Level 21

New level


25 words 0 ignored

Ready to learn       Ready to review

Ignore words

Check the boxes below to ignore/unignore words, then click save at the bottom. Ignored words will never appear in any learning session.

All None

Ignore?
Malaya
Shirt
Ndidzakugulira malaya
I will buy you a shirt
Chisoti
Hat
Sokosi
Sock
Buluku
Trousers
Kuvala mabuluku
Wearing trousers
Amene
Who / that (m/ma/a class)
Mwana amene akupita
The child who is going
Kuyimba
To sing
Anthu amene akuyimba
The people who are singing
Galu amene akudya
The dog that is eating
Mabuku amene ndinagula
The books that I bought
Kuonetsa
To show
Anonetsa chimwemwe ndi chikondi
They showed joy and love (=they were happy)
Kutsata kuti
So that / following on that
Kutsata nzeru zatsopano
Following modern wisdom
Mayeso
Exams
Masamu
Maths
Kuvuta
To be difficult
Masamu wovuta
Difficult sums
Ndi wovuta kuwasamala
It is difficult to handle
Nkosavuta kunena kuti
It is not difficult to say that
Kuphweka
To be easy
Mayeso adzakhala ophweka
The exams are going to be easy
Masamu sanali ophweka
The sums were not easy