Level 24 Level 26
Level 25

New level


24 words 0 ignored

Ready to learn       Ready to review

Ignore words

Check the boxes below to ignore/unignore words, then click save at the bottom. Ignored words will never appear in any learning session.

All None

Ignore?
Lachisanu
Friday
Loweruka
Saturday
Tidzachite chiyani pa loweruka?
What shall we do on Saturday?
Lopumula
Sunday
Kuwerenga
To read
Wopereka zakudya
Waiter / Waitress (lit-provider of food)
Wophika
Cook
Wonena
Speaker
Woopsa
Dangerous person
Wopanda
Person having nothing
Wopanda pa ntchito
Unemployed person
Wopanda nzeru
Unwise / empty headed person
Edzi
AIDS
Kachilombo
Bacteria / virus / parasite /small insect
Akudandaula za chitetezo cha ana ake
He is worried about the safety of his children
Ana amafuna chikondi ndi chitetezo
Children need love & security
Chitetezo cha m'thupi
Body immunity
Chitetezo cha ana ku matenda
Children's Immunisation
Kusowa chitetezo cha m'thupi
Immunodeficiency
Kachilombo kochepetsa chitetezo m'thupi
HIV
Kuchepetsa
To decrease / lessen
Kuchepetsa umphawi
Alleviate poverty
Ndizachepetsa mpata
I will lessen the gap
Mpata
Space / gap / time / room