Level 3 Level 5
Level 4

Chi- Z- (Nouns)


283 words 0 ignored

Ready to learn       Ready to review

Ignore words

Check the boxes below to ignore/unignore words, then click save at the bottom. Ignored words will never appear in any learning session.

All None

Ignore?
chabodza
fake
chachikale
old thing
chachikhalire
that which has always existed
chachikuda
African matter
chachikulu
provided
chachikunja
secular thing; irreligious thing
chachilendo
strange thing
chaka
year
chakudya
food
chakudza
event
chakumwa
drink
chakunja
exterior
chala
finger; toe
chalusi
numbness
cham'kati
interior
chenjezo
warning; caution
chibabwidwe
nature
chibadwa
natural disposition; something hereditary
chibadwidwe
the way one is by birth
chibakera
fist
chibale
state of being a relative
chibalima
freckle
chibaliro
womb (1)
chibalo
punishment; penalty; consequence
chibayiro
stake
chibayo
pneumonia
chiberekero
uterus
chibisibisi
secrecy
chiboolera
drill; thing that makes holes
chibwano
chin
chibwenzi
friendship; romance
chibwereza
repetition
chida
tool; implement
chidakwa
drunkard
chidalala
rocky soil
chidani
hatred; enmity
chidebe
large tin; pail
chidede
leafy relish like okra
chidole
doll
chidude
spirit of a dead person; ghost
chidule
shortness; summary; shortcut
chidutswa
scrap; broken piece
chidwi
interest; curiosity
chidyerano
sharing food together
chidziwitso
knowledge
chifanifani
similar thing
chifaniziro
likeness; reference
chifanizo
image; representation
chifukwa
reason
chifundo
kindness; mercy
chifuniro
will; wish; desire
chifupikitso
summary; abbreviation; shortened thing
chifuwa
chest; cough
chigamba
patch
chigandanga
armed robber; gangster
chiganizo
sentence; complete thought
chigawo
region
chigayo
maize mill
chigongono
elbow
chigono
night (on a journey)
chigwa
valley; low place
chigwiriro
handle
chigwirizano
cooperation; agreement
chikande
yam
chikasu
yellow
chikayiko
doubt; mistrust
chikhadabo
fingernail; claw (1)
chikhalidwe
way of life; character; conduct
chikhaliro
that on which something rests or sits; bottom; base; support
chikhazikitso
an assuring thing
chikho
gourd
chikhomo
peg
chikhulupiriro
faith; confidence; belief
chikoka
attraction; appeal
chikole
gift given to obligate a return gift; pledge
chikolopa
mop; cloth
chikometsamlandu
bribe; corruption at court
chikometsero
decoration
chikondano
mutual love; neighbourly love
chikondi
love
chikondwerero
feast; joy; happiness
chikonzekero
preparation; readiness
chikonzero
plan; preparation; decision
chikopa
animal hide
chikope
eyelid
chikoti
whip
chikuku
measles
chikumbukiro
memory; remembrance
chikumbumtima
conscience; memory
chikumbutso
monument; memorial; reminder
chikuta
new-born baby's first days
chikutiro
wrapping material; wrapper
chikwama
bag; wallet
chikwanje
panga knife
chikwati
wedding
chikwera
elevation
chilakolako
desire
chilala
drought
chilamulo
law
chilango
punishment
chilankhulo
language
chilembo
letter; character
chilembwe
roan antelope
chilemekezo
honour; exaltation
chilendo
strangeness; foreignness
chilengedwe
nature; natural
chilichonse
anything
chilimbikitso
strength; encouragement; support
chilimwe
hot; dry season when hoeing is done
chiliro
mourning; weeping
chilolezo
permit; licence; permission
chilombo
wild beast; wild animal
chilonjezo
promise
chilumba
island
chilumika
year (Chitumbuka)
chilundu
cloth for wrapping around the body
chilungamo
righteousness; justice
chimaliziro
ending
chimanga
maize
chimangirizo
composition; essay
chimbudzi
latrine; toilet
chimdidi
women's dance
chimera
sprouted maize
chimfine
head cold
chimphuli
large pot for storing ufa
chimunthu
crowd; giant
chimvano
alliance; league; concord
chimwemwe
joy
chinanazi
pineapple
chinangwa
cassava
chinansi
neighbourliness; relationship
chindapusa
fine; payment
chinenero
speech; language
chingerezi
English language
chingwe
string; rope
chinsinsi
secret
chinthu
thing; object
chinyalala
rubbish
chinyengo
fraud; deceit
chinyezi
moisture
chinyoto
moisture (2)
chionetsero
show; showing off
chiongoladzanja
interest (money)
chiongolero
steering wheel
chionongeko
destruction
chipalamba
infertile place; dry place
chipalapasiro
chicken leg
chipalawo
paddle for dugout
chipale
shallow place; sandbank in lake
chipaliwali
lightning (1)
chipambano
victory; excellence
chipande
wooden spoon
chipangano
agreement; contract
chipangizo
tool; instrument
chipani
political party
chipata
gate
chipatala
hospital; clinic
chipatso
fruit
chipembedzo
religion; worship; faith
chipepeso
condolence
chipere
mashed beans
chipeso
comb (n)
chipewa
hat
chiphaso
permit; ticket
chiphe
poison
chiphetsa
a very beautiful woman
chiphona
giant; strong person
chiphunzitso
teaching; doctrine
chiphuphu
bribe; pimple
chipima
scales
chipinda
room
chipolopolo
bullet
chipondamthengo
payment to herbalist; deposit money
chipondero
sole of foot; hoof
chipongwe
insolence rudeness
chipsera
scar; scab; burn
chipsyera
scar; burn
chipululu
desert; dry land
chipulumutso
salvation
chipupa
wall; dyke
chiputa
rudeness
chiputu
grass thicket; stage in girls initiation
chipwirikiti
disorder; violence; mob
chipwitikizi
Portuguese language
chirimwe
dry season
chirombo
wild beast; creature
chironda
wound; sore
chisa
nest
chisamaliro
care
chisambiro
sponge; thing to wash with
chisangalalo
fun; good time
chisankho
choice; election; vote
chisanu
cold season
chisautso
suffering; burden
chisavomerezo
disagreement
chisawawa
chaos; disorder
chisikiro
sickle
chisilamu
Islam
chisiriro
covetousness
chisokonezo
mess; confusion; disturbance
chisoni
sadness; sorrow; pity
chisoso
black jack
chiswe
termite
chitamba
elephant's trunk
chitambaya
shawl; handkerchief
chitanda
dead body; corpse (1)
chitanga
coop for fowls
chitayiko
lostness; perdition
chitayo
abortion; miscarriage; miscarried baby
chitendene
heel
chitengero
vessel; carrier
chitengwa
taking wife to stay with man's family
chitetero
statement
chithandala
drying rack
chithandizo
help; aid; assistance
chithokozo
thanks
chithunzi
picture
chithupsa
abscess; swelling
chitsa
tree stump
chitsanzo
example
chitseko
door
chitsime
well
chitsiru
fool (1)
chitsononkho
maize cob
chitsotso
specks
chitsulo
iron; piece or thing made of metal
chitukuko
development (n)
chitundu
big basket
chiuno
hip; waist
chivomerezo
agreement; confession
chivomezi
earth tremor
chiwala
grasshopper
chiwalo
limb; part of body
chiwanda
ghost
chiwawa
noise
chiwembu
grudge
chiwerengero
number; count of something
chiwerewere
promiscuity
chiweruzo
judgment
chiweto
livestock
chiwindi
liver
chiwira
system of communal labour
chiwiya
kitchen utensil
chiwongo
dowry
chiyambi
beginning
chiyamiko
compliment
chiyanjanitso
thing that reconciles; reconciliation
chiyanjano
communion; fellowship
chiyembekezo
hope; expectation
chiyerekezo
assumption; imagination; guess
chiyeretso
sanctification
chiyero
holiness; purity
chizindikiritso
assurance
chizindikiro
sign; symbol
chizolowezi
habit; custom
chizungulire
dizziness
chobedwa
stolen thing
chochitika
event
chochititsa
cause (n)
chodabwitsa
extraordinary thing
chofunda
bedding
choipa
misdeed
chokolo
custom - widow marries into husbands family
cholakalaka
need; want
cholakwa
mistake
cholembera
pen; pencil
cholengedwa
creature; creation; nature
cholinga
aim; intention; purpose
cholobodoka
soft thing; weakling
cholondola
correct thing; exact thing
choluma
biting insect; wild beast
chombo
ship; big boat
choopsa
dangerous thing; fearful thing
chosalungama
crime; sin; injustice
chotengera
bag
chotsatira
by-product; aftermath; result
chotupa
swelling bruise
chovala
piece of clothing; dress
chovuta
difficulty; difficult thing
chowona
truth
choyankha
answer; response
chule
frog
zinthu zapadera
spares; extra items (pl)