Level 7 Level 9
Level 8

Adjectives


113 words 0 ignored

Ready to learn       Ready to review

Ignore words

Check the boxes below to ignore/unignore words, then click save at the bottom. Ignored words will never appear in any learning session.

All None

Ignore?
basi
enough; that’s all
bwino
well; fine; later on
-bwino
good; kind
bwino!
mind
chabe
adv. only; just/ adj. worthless; vain
-chabe
worthless
chagada
on the back; supine
chahcikulu
huge
-chete
silent
-chilendo
foreign
chilili
upright (standing); as it is
chimodzimodzi
the same; like before
chire
ready
chonchi
like this
choncho
like that; so-so
chondondozana
in single file
choyamba
first of all; to begin with
dala
on purpose; deliberately (1)
fufumimba
on the belly; prone
kachetechete
silently
-kale
old; former
kapena
either or; perhaps
kaya
I don't know; perhaps
koposa
most; very much
kosalekeza
continuously
kuposa
more than
kutengera ndi
according to
kwabasi
very much; a lot
kwambiri
much; very; a lot
kwathunthu
entirely
kwenikweni
especially; real; really
makamaka
especially
-makono
modern times
malinga ndi
(adverb) since; according to; seeing as
malingana ndi
in accordance; according to
-mangamanga
tied up
-mapasa
twin
maso
awake
mawanga akuda ndi oyera
black and white
mawangamawanga
multi-coloured
-mbiri
many
mizeremizere
striped
m'malo mwa
instead of (noun)
mmodzimmodzi
one by one
modekha
calmly
mokwanira
enough
molakwika
badly; wrongly
molimba
industriously; boldly
mommuja
as before; no change
monga
like; such as
monga mmene
in the same way that
monyada
proudly
mopanda ulemu
impolitely
mopeneka
doubtfully
mosafulumira
without haste
mosakhalitsa
without delay
mosamala
carefully (2)
motero kuti
so that (result)
mothamanga
speedily
-mphamvu
healthy; strong
-mphongo
male (ad)
-mphuluphulu
naughty
msangamsanga
very fast
mseri
privately; secretly
mwa chizolwezi
as usual
mwa mwayi
luckily
mwachidule
for short
mwachitsanzo
for example
mwadala
on purpose; deliberately (2)
mwadzidzidzi
suddenly
mwangozi
by accident
-mwano
rude
mwatsoka
unfortunately
mwaufulu
freely
mwaulemu
politely
-mwayi
lucky
mwina
maybe
mwinamwake
possibly; maybe
ndithu
indeed
ndithudi
indeed; without a doubt
-ngapo
a fair number of
ngati
like; as if
-njiru
jealous
-onga
similar
-padera
spare; out of place
-pafupi
easy; nearby
pafupifupi
almost; nearly
pafupipafupi
close together; one after the other
pamodzi
together
pang'ono
a little
pang'ono-ng'ono
about to; nearly
pang'ono-pang'ono
slowly
-patali
difficult
penipeni
right; exactly
pozembera
alibi
-thanzi
burly; well built
-thunthu
full; whole
tsonga
upright; straight (sitting)
tsono
so; now ; at the moment
-tsopano
new; modern
udyo
badly
ulere
free of charge
-uve
scruffy; dirty
-wira
boiling
wonga
like
zedi
really (emphasis)
zingapo
a fair number
ziwiriziwiri
two by two
zololedwa
legal; lawful
zoona
true
zoonadi
truly; indeed
zosachepera
not less than
zosaloledwa
illegal; unlawful